Luka 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anachitanso chimodzimodzi ndi kapu+ atadya chakudya chamadzulocho. Iye anati: “Kapu iyi ikutanthauza pangano latsopano+ pamaziko a magazi anga,+ amene adzakhetsedwa chifukwa cha inu.+
20 Anachitanso chimodzimodzi ndi kapu+ atadya chakudya chamadzulocho. Iye anati: “Kapu iyi ikutanthauza pangano latsopano+ pamaziko a magazi anga,+ amene adzakhetsedwa chifukwa cha inu.+