Yeremiya 31:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Taonani! Masiku adzafika, pamene ndidzachita pangano latsopano+ ndi nyumba ya Isiraeli+ komanso ndi nyumba ya Yuda,”+ watero Yehova. Yeremiya 32:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndidzachita nawo pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale+ lakuti sindidzasiya kuwachitira zabwino+ ndipo ndidzawapatsa mtima woti azindiopa kuti asachoke kwa ine.+ 2 Akorinto 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ndipo chifukwa cha iyeyo ndife oyenera kukhala atumiki a pangano latsopano,+ ndipo ndife ogwirizana osati kudzera m’malamulo olembedwa,+ koma mu mzimu.+ Pakuti malamulo olembedwa amaweruza munthu+ kuti afe, koma mzimu umapatsa munthu moyo.+ Aheberi 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa chifukwa chimenecho, Yesu wakhala chikole cha pangano labwino koposa.+ Aheberi 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti iye akuimba anthu mlandu pamene akunena kuti: “‘Taonani! Masiku adzafika, pamene ndidzachita pangano latsopano ndi nyumba ya Isiraeli komanso ndi nyumba ya Yuda,’ watero Yehova.+
31 “Taonani! Masiku adzafika, pamene ndidzachita pangano latsopano+ ndi nyumba ya Isiraeli+ komanso ndi nyumba ya Yuda,”+ watero Yehova.
40 Ndidzachita nawo pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale+ lakuti sindidzasiya kuwachitira zabwino+ ndipo ndidzawapatsa mtima woti azindiopa kuti asachoke kwa ine.+
6 ndipo chifukwa cha iyeyo ndife oyenera kukhala atumiki a pangano latsopano,+ ndipo ndife ogwirizana osati kudzera m’malamulo olembedwa,+ koma mu mzimu.+ Pakuti malamulo olembedwa amaweruza munthu+ kuti afe, koma mzimu umapatsa munthu moyo.+
8 Pakuti iye akuimba anthu mlandu pamene akunena kuti: “‘Taonani! Masiku adzafika, pamene ndidzachita pangano latsopano ndi nyumba ya Isiraeli komanso ndi nyumba ya Yuda,’ watero Yehova.+