Ezekieli 36:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndidzakupatsani mtima watsopano,+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa inu.+ Ndidzakuchotserani mtima wanu wamwala n’kukupatsani mtima wamnofu.+ Chivumbulutso 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi ndani sadzakuopani,+ inu Yehova?+ Ndani sadzalemekeza dzina lanu?+ Pakuti inu nokha ndinu wokhulupirika.+ Mitundu yonse ya anthu idzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa malamulo anu olungama aonekera.”+
26 Ndidzakupatsani mtima watsopano,+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa inu.+ Ndidzakuchotserani mtima wanu wamwala n’kukupatsani mtima wamnofu.+
4 Kodi ndani sadzakuopani,+ inu Yehova?+ Ndani sadzalemekeza dzina lanu?+ Pakuti inu nokha ndinu wokhulupirika.+ Mitundu yonse ya anthu idzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa malamulo anu olungama aonekera.”+