Salimo 73:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 73 Mulungu ndi wabwinodi kwa Isiraeli, kwa anthu oyera mtima.+ Salimo 125:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu Yehova, chitirani zabwino anthu abwino,+Anthu owongoka mtima.+ Ezekieli 39:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Sindidzawabisiranso nkhope yanga+ chifukwa panyumba ya Isiraeli, ndidzatsanulirapo mzimu wanga,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
29 Sindidzawabisiranso nkhope yanga+ chifukwa panyumba ya Isiraeli, ndidzatsanulirapo mzimu wanga,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”