Mateyu 26:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamene anali kudya, Yesu anatenga mkate,+ ndipo atapempha dalitso, anaunyemanyema+ n’kuupereka kwa ophunzira ake. Iye anati: “Eni, idyani. Mkate uwu ukuimira thupi langa.”+ Luka 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako anatenga mkate.+ Atayamika anaunyemanyema n’kuwapatsa, ndipo anati: “Mkate uwu ukuimira thupi langa+ limene likuperekedwa chifukwa cha inu.+ Muzichita zimenezi pondikumbukira.”+
26 Pamene anali kudya, Yesu anatenga mkate,+ ndipo atapempha dalitso, anaunyemanyema+ n’kuupereka kwa ophunzira ake. Iye anati: “Eni, idyani. Mkate uwu ukuimira thupi langa.”+
19 Kenako anatenga mkate.+ Atayamika anaunyemanyema n’kuwapatsa, ndipo anati: “Mkate uwu ukuimira thupi langa+ limene likuperekedwa chifukwa cha inu.+ Muzichita zimenezi pondikumbukira.”+