Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “‘Adzadye nyamayo usiku umenewu.+ Idzakhale yowotcha ndipo adzaidye pamodzi ndi mikate yopanda chofufumitsa+ ndi masamba owawa.+

  • Ekisodo 12:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Musamadzadye chilichonse chokhala ndi chofufumitsa. M’nyumba zanu zonse muzidzadya mikate yopanda chofufumitsa.’”

  • Deuteronomo 16:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Usadye nsembeyo pamodzi ndi chilichonse chokhala ndi chofufumitsa. Masiku 7+ uzidya mkate wopanda chofufumitsa, umene ndi mkate wa nsautso, chifukwa unatuluka mofulumira m’dziko la Iguputo.+ Uzichita zimenezi kuti uzikumbukira tsiku limene unatuluka m’dziko la Iguputo, masiku onse a moyo wako.+

  • 1 Akorinto 10:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Popeza pali mkate umodzi, ifeyo, ngakhale kuti tilipo ambiri,+ ndife thupi limodzi,+ pakuti tonse tikudya nawo mkate umodziwo.+

  • 1 Akorinto 11:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pakuti zimene ndinalandira kwa Ambuye n’zimene inenso ndinakupatsirani, zakuti Ambuye Yesu, usiku+ umene anali kukaperekedwa anatenga mkate.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena