Mateyu 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nthawi yamadzulo,+ iye ndi ophunzira ake 12 aja anali kudya chakudya patebulo.+ Luka 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Nthawi itakwana, anakhala patebulo la chakudya, atumwi akenso anali naye limodzi.+