Mateyu 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nthawi yamadzulo,+ iye ndi ophunzira ake 12 aja anali kudya chakudya patebulo.+ Maliko 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chakumadzulo ndithu, Yesu anafika limodzi ndi ophunzira ake 12 aja.+