Mateyu 26:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamene anali kudya, Yesu anatenga mkate,+ ndipo atapempha dalitso, anaunyemanyema+ n’kuupereka kwa ophunzira ake. Iye anati: “Eni, idyani. Mkate uwu ukuimira thupi langa.”+ Maliko 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamene anali kudya, iye anatenga mkate ndi kupempha dalitso. Kenako anaunyemanyema ndi kuwapatsa, ndipo anati: “Tengani, mkate uwu ukuimira thupi langa.”+ 1 Akorinto 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo atayamika, anaunyemanyema+ n’kunena kuti: “Mkate uwu ukuimira thupi langa+ limene likuperekedwa chifukwa cha inu. Muzichita zimenezi pondikumbukira.”+
26 Pamene anali kudya, Yesu anatenga mkate,+ ndipo atapempha dalitso, anaunyemanyema+ n’kuupereka kwa ophunzira ake. Iye anati: “Eni, idyani. Mkate uwu ukuimira thupi langa.”+
22 Pamene anali kudya, iye anatenga mkate ndi kupempha dalitso. Kenako anaunyemanyema ndi kuwapatsa, ndipo anati: “Tengani, mkate uwu ukuimira thupi langa.”+
24 Ndipo atayamika, anaunyemanyema+ n’kunena kuti: “Mkate uwu ukuimira thupi langa+ limene likuperekedwa chifukwa cha inu. Muzichita zimenezi pondikumbukira.”+