Maliko 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamene anali kudya, iye anatenga mkate ndi kupempha dalitso. Kenako anaunyemanyema ndi kuwapatsa, ndipo anati: “Tengani, mkate uwu ukuimira thupi langa.”+ Luka 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako anatenga mkate.+ Atayamika anaunyemanyema n’kuwapatsa, ndipo anati: “Mkate uwu ukuimira thupi langa+ limene likuperekedwa chifukwa cha inu.+ Muzichita zimenezi pondikumbukira.”+
22 Pamene anali kudya, iye anatenga mkate ndi kupempha dalitso. Kenako anaunyemanyema ndi kuwapatsa, ndipo anati: “Tengani, mkate uwu ukuimira thupi langa.”+
19 Kenako anatenga mkate.+ Atayamika anaunyemanyema n’kuwapatsa, ndipo anati: “Mkate uwu ukuimira thupi langa+ limene likuperekedwa chifukwa cha inu.+ Muzichita zimenezi pondikumbukira.”+