Aheberi 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwa “chifuniro”+ chimenecho, tayeretsedwa+ kudzera m’thupi la Yesu Khristu loperekedwa nsembe+ kamodzi+ kokha. 1 Petulo 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iye ananyamula machimo athu+ m’thupi lake pamtengo,+ kuti tilekane ndi machimo+ n’kukhala amoyo m’chilungamo. Ndipo “munachiritsidwa ndi mabala ake.”+
10 Mwa “chifuniro”+ chimenecho, tayeretsedwa+ kudzera m’thupi la Yesu Khristu loperekedwa nsembe+ kamodzi+ kokha.
24 Iye ananyamula machimo athu+ m’thupi lake pamtengo,+ kuti tilekane ndi machimo+ n’kukhala amoyo m’chilungamo. Ndipo “munachiritsidwa ndi mabala ake.”+