Yohane 6:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Ine ndine chakudya chamoyo chotsika kumwamba. Ngati wina adyako chakudya chimenechi adzakhala ndi moyo kosatha. Ndipotu chakudya chimene ndidzapereke kuti dzikoli lipeze moyo,+ ndicho mnofu wangawu.”+ 1 Akorinto 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi kapu+ ya dalitso imene timadalitsa, sitanthauza kugawana magazi a Khristu?+ Kodi mkate umene timanyema,+ sutanthauza kugawana thupi la Khristu?
51 Ine ndine chakudya chamoyo chotsika kumwamba. Ngati wina adyako chakudya chimenechi adzakhala ndi moyo kosatha. Ndipotu chakudya chimene ndidzapereke kuti dzikoli lipeze moyo,+ ndicho mnofu wangawu.”+
16 Kodi kapu+ ya dalitso imene timadalitsa, sitanthauza kugawana magazi a Khristu?+ Kodi mkate umene timanyema,+ sutanthauza kugawana thupi la Khristu?