Mateyu 26:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako anatenga kapu+ ndipo atayamika, anaipereka kwa iwo n’kunena kuti: “Imwani nonsenu.+ Yohane 6:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Choncho Yesu anawauza kuti: “Ndithudi ndikukuuzani, Mukapanda kudya mnofu+ wa Mwana wa munthu ndi kumwa magazi ake,+ mulibe moyo+ mwa inu. 1 Akorinto 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi kapu+ ya dalitso imene timadalitsa, sitanthauza kugawana magazi a Khristu?+ Kodi mkate umene timanyema,+ sutanthauza kugawana thupi la Khristu? 1 Akorinto 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Anachitanso chimodzimodzi ndi kapu+ atadya chakudya chamadzulo, ndipo anati: “Kapu iyi ikutanthauza pangano latsopano+ pamaziko a magazi anga.+ Muzichita zimenezi nthawi zonse pamene mukumwa za m’kapu imeneyi pondikumbukira.”+
53 Choncho Yesu anawauza kuti: “Ndithudi ndikukuuzani, Mukapanda kudya mnofu+ wa Mwana wa munthu ndi kumwa magazi ake,+ mulibe moyo+ mwa inu.
16 Kodi kapu+ ya dalitso imene timadalitsa, sitanthauza kugawana magazi a Khristu?+ Kodi mkate umene timanyema,+ sutanthauza kugawana thupi la Khristu?
25 Anachitanso chimodzimodzi ndi kapu+ atadya chakudya chamadzulo, ndipo anati: “Kapu iyi ikutanthauza pangano latsopano+ pamaziko a magazi anga.+ Muzichita zimenezi nthawi zonse pamene mukumwa za m’kapu imeneyi pondikumbukira.”+