Mlaliki 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ine ndinafuna kumvetsetsa ndi kuganizira mozama zinthu zonsezi:+ Anthu olungama ndiponso anthu anzeru limodzi ndi ntchito zawo ali m’dzanja la Mulungu woona.+ Anthu sadziwa za chikondi kapena chidani chimene chinalipo iwo asanakhalepo.+ Maliro 3:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Tsopano ndani ananenapo kuti chinthu chichitike, chinthucho n’kuchitikadi Yehova asanalamule?+ Yakobo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 M’malomwake, muyenera kunena kuti: “Yehova akalola,+ tikhala ndi moyo, ndi kuchita zakutizakuti.”+
9 Ine ndinafuna kumvetsetsa ndi kuganizira mozama zinthu zonsezi:+ Anthu olungama ndiponso anthu anzeru limodzi ndi ntchito zawo ali m’dzanja la Mulungu woona.+ Anthu sadziwa za chikondi kapena chidani chimene chinalipo iwo asanakhalepo.+
15 M’malomwake, muyenera kunena kuti: “Yehova akalola,+ tikhala ndi moyo, ndi kuchita zakutizakuti.”+