Salimo 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzadzitamandira mwa Yehova.+Ofatsa adzamva ndi kukondwera.+ Aheberi 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu akalola, tiyesetsadi mwakhama kuti tikhale okhwima mwauzimu.+