Yakobo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 M’malomwake, muyenera kunena kuti: “Yehova akalola,+ tikhala ndi moyo, ndi kuchita zakutizakuti.”+
15 M’malomwake, muyenera kunena kuti: “Yehova akalola,+ tikhala ndi moyo, ndi kuchita zakutizakuti.”+