Salimo 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimakondwera ndi kuchita chifuniro chanu, inu Mulungu wanga,+Ndipo chilamulo chanu chili mumtima mwanga.+ Salimo 143:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiphunzitseni kuchita chifuniro chanu,+Pakuti inu ndinu Mulungu wanga.+Mzimu wanu ndi wabwino.+Unditsogolere m’dziko la olungama.+ Yohane 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yesu anati: “Chakudya+ changa ndicho kuchita chifuniro+ cha amene anandituma ndi kutsiriza ntchito yake.+ Machitidwe 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 M’malomwake, anatsanzikana+ nawo ndi kuwauza kuti: “Yehova akalola ndidzabweranso kudzakuonani.”+ Choncho ananyamuka ku Efeso ulendo wa panyanja
8 Ndimakondwera ndi kuchita chifuniro chanu, inu Mulungu wanga,+Ndipo chilamulo chanu chili mumtima mwanga.+
10 Ndiphunzitseni kuchita chifuniro chanu,+Pakuti inu ndinu Mulungu wanga.+Mzimu wanu ndi wabwino.+Unditsogolere m’dziko la olungama.+
34 Yesu anati: “Chakudya+ changa ndicho kuchita chifuniro+ cha amene anandituma ndi kutsiriza ntchito yake.+
21 M’malomwake, anatsanzikana+ nawo ndi kuwauza kuti: “Yehova akalola ndidzabweranso kudzakuonani.”+ Choncho ananyamuka ku Efeso ulendo wa panyanja