Salimo 55:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Umutulire Yehova nkhawa zako,+Ndipo iye adzakuchirikiza.+Sadzalola kuti wolungama agwedezeke.+ Miyambo 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pereka ntchito zako kwa Yehova,+ ndipo zolinga zako ndithu zidzakhazikika.+