2 Samueli 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Pita, ukauze mtumiki wanga Davide kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Kodi iwe ungandimangire nyumba yoti ine ndikhalemo?+ 2 Samueli 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye ndi amene adzamangira dzina langa nyumba,+ ndipo ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mpaka kalekale.+
5 “Pita, ukauze mtumiki wanga Davide kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Kodi iwe ungandimangire nyumba yoti ine ndikhalemo?+
13 Iye ndi amene adzamangira dzina langa nyumba,+ ndipo ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mpaka kalekale.+