Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 5:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Inuyo mukudziwa bwino kuti Davide bambo anga sanathe kumanga nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wake, chifukwa cha nkhondo+ zimene adani ake ankamenyana naye m’madera onse omuzungulira, mpaka pamene Yehova anaika adani akewo pansi pa mapazi ake.

  • 1 Mafumu 8:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma iweyo sumanga nyumbayi, m’malomwake mwana wako wamwamuna wotuluka m’chiuno mwako ndi amene adzamange nyumba ya dzina langa.’+

  • 1 Mbiri 17:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Pita, ukauze Davide mtumiki wanga kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Si iwe amene udzandimangira nyumba yokhalamo.+

  • 1 Mbiri 22:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma mawu a Yehova ananditsutsa, kuti: ‘Iweyo wakhetsa magazi ambirimbiri+ ndipo wamenya nkhondo zikuluzikulu.+ Sungamange nyumba ya dzina langa,+ chifukwa wakhetsa magazi ambirimbiri pamaso panga padziko lapansi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena