1 Mbiri 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Pita, ukauze Davide mtumiki wanga kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Si iwe amene udzandimangira nyumba yokhalamo.+ 2 Mbiri 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma iweyo sumanga nyumbayi,+ m’malomwake mwana wako wamwamuna wotuluka m’chiuno mwako ndi amene adzamange nyumba ya dzina langa.’+
4 “Pita, ukauze Davide mtumiki wanga kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Si iwe amene udzandimangira nyumba yokhalamo.+
9 Koma iweyo sumanga nyumbayi,+ m’malomwake mwana wako wamwamuna wotuluka m’chiuno mwako ndi amene adzamange nyumba ya dzina langa.’+