2 Samueli 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Pita, ukauze mtumiki wanga Davide kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Kodi iwe ungandimangire nyumba yoti ine ndikhalemo?+ 1 Mafumu 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma iweyo sumanga nyumbayi, m’malomwake mwana wako wamwamuna wotuluka m’chiuno mwako ndi amene adzamange nyumba ya dzina langa.’+ 1 Mbiri 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma mawu a Yehova ananditsutsa, kuti: ‘Iweyo wakhetsa magazi ambirimbiri+ ndipo wamenya nkhondo zikuluzikulu.+ Sungamange nyumba ya dzina langa,+ chifukwa wakhetsa magazi ambirimbiri pamaso panga padziko lapansi.
5 “Pita, ukauze mtumiki wanga Davide kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Kodi iwe ungandimangire nyumba yoti ine ndikhalemo?+
19 Koma iweyo sumanga nyumbayi, m’malomwake mwana wako wamwamuna wotuluka m’chiuno mwako ndi amene adzamange nyumba ya dzina langa.’+
8 Koma mawu a Yehova ananditsutsa, kuti: ‘Iweyo wakhetsa magazi ambirimbiri+ ndipo wamenya nkhondo zikuluzikulu.+ Sungamange nyumba ya dzina langa,+ chifukwa wakhetsa magazi ambirimbiri pamaso panga padziko lapansi.