2 Samueli 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Pita, ukauze mtumiki wanga Davide kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Kodi iwe ungandimangire nyumba yoti ine ndikhalemo?+ 1 Mbiri 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma mawu a Yehova ananditsutsa, kuti: ‘Iweyo wakhetsa magazi ambirimbiri+ ndipo wamenya nkhondo zikuluzikulu.+ Sungamange nyumba ya dzina langa,+ chifukwa wakhetsa magazi ambirimbiri pamaso panga padziko lapansi. 2 Mbiri 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Yehova anauza Davide bambo anga kuti, ‘Popeza unafuna mumtima mwako kumanga nyumba ya dzina langa, unachita bwino chifukwa unafuna mumtima mwako kuchita zimenezi.+
5 “Pita, ukauze mtumiki wanga Davide kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Kodi iwe ungandimangire nyumba yoti ine ndikhalemo?+
8 Koma mawu a Yehova ananditsutsa, kuti: ‘Iweyo wakhetsa magazi ambirimbiri+ ndipo wamenya nkhondo zikuluzikulu.+ Sungamange nyumba ya dzina langa,+ chifukwa wakhetsa magazi ambirimbiri pamaso panga padziko lapansi.
8 Koma Yehova anauza Davide bambo anga kuti, ‘Popeza unafuna mumtima mwako kumanga nyumba ya dzina langa, unachita bwino chifukwa unafuna mumtima mwako kuchita zimenezi.+