Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 37:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Lola kuti Yehova akutsogolere panjira yako,+

      Umudalire+ ndipo iye adzachitapo kanthu.+

  • Salimo 55:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Umutulire Yehova nkhawa zako,+

      Ndipo iye adzakuchirikiza.+

      Sadzalola kuti wolungama agwedezeke.+

  • Mateyu 6:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 “Chotero pitirizani kufunafuna ufumu choyamba ndi chilungamo chake,+ ndipo zina zonsezi zidzawonjezedwa kwa inu.+

  • Afilipi 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Musamade nkhawa ndi kanthu kalikonse,+ koma pa chilichonse, mwa pemphero ndi pembedzero,+ pamodzi ndi chiyamiko, zopempha zanu zidziwike kwa Mulungu.+

  • 1 Petulo 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chitani zimenezi pamene mukumutulira nkhawa zanu zonse,+ pakuti amakuderani nkhawa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena