Salimo 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+Popeza kuti ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.+ Salimo 37:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ngakhale atapunthwa, sadzagweratu,+Pakuti Yehova wamugwira dzanja.+ Salimo 62:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye ndiye thanthwe langa ndi chipulumutso changa, malo anga okwezeka ndiponso achitetezo.+Sindidzagwedezeka kwambiri.+ Salimo 121:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye sangalole kuti phazi lako lipunthwe.+Amene amakuyang’anira sangawodzere.+
8 Ndaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+Popeza kuti ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.+
2 Iye ndiye thanthwe langa ndi chipulumutso changa, malo anga okwezeka ndiponso achitetezo.+Sindidzagwedezeka kwambiri.+