1 Samueli 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mapazi a okhulupirika ake amawateteza.+Koma anthu oipa amawawononga mu mdima,+Pakuti munthu sakhala wapamwamba chifukwa cha mphamvu zake.+ Salimo 91:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo adzakunyamula m’manja mwawo,+Kuti phazi lako lisawombe mwala uliwonse.+ Miyambo 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti Yehova ndiye amene uzidzamudalira,+ ndipo adzateteza phazi lako kuti lisakodwe.+ Luka 1:79 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 79 ndipo kudzaunikira amene akhala mu mdima ndi mu mthunzi wa imfa,+ ndi kutsogolera bwinobwino mapazi athu panjira yamtendere.”
9 Mapazi a okhulupirika ake amawateteza.+Koma anthu oipa amawawononga mu mdima,+Pakuti munthu sakhala wapamwamba chifukwa cha mphamvu zake.+
79 ndipo kudzaunikira amene akhala mu mdima ndi mu mthunzi wa imfa,+ ndi kutsogolera bwinobwino mapazi athu panjira yamtendere.”