Salimo 139:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nditati ndiyese kuwawerenga, angakhale ochuluka kwambiri kuposa mchenga.+Podzuka ndingakhale ndikuwawerengabe.+ Machitidwe 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ponena za iyeyu, pajatu Davide anati, ‘Ndinali kuona Yehova patsogolo panga nthawi zonse. Popeza kuti ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka ngakhale pang’ono.+
18 Nditati ndiyese kuwawerenga, angakhale ochuluka kwambiri kuposa mchenga.+Podzuka ndingakhale ndikuwawerengabe.+
25 Ponena za iyeyu, pajatu Davide anati, ‘Ndinali kuona Yehova patsogolo panga nthawi zonse. Popeza kuti ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka ngakhale pang’ono.+