Salimo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ine ndidzagona pansi ndi kupeza tulo.Ndidzadzuka ndithu, pakuti Yehova amandithandiza.+ Salimo 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ine ndidzaona nkhope yanu m’chilungamo.+Podzuka, ndidzakhutira pokuonani.+ Salimo 63:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndikakumbukira inu ndili pabedi langa,+Pa nthawi za ulonda wa usiku* ndimasinkhasinkha za inu.+