Salimo 119:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Usiku ndimakumbukira dzina lanu, inu Yehova,+Kuti ndisunge chilamulo chanu.+ Salimo 119:148 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 148 Ndimadzuka pa ulonda wa usiku,+Kuti ndisinkhesinkhe mawu anu.+