Salimo 42:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Masana Yehova adzalamula kukoma mtima kwake kosatha kuti kufike pa ine,+Ndipo usiku ndidzaimba za iye.+Ndidzapemphera kwa Mulungu wondipatsa moyo.+ Salimo 63:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndikakumbukira inu ndili pabedi langa,+Pa nthawi za ulonda wa usiku* ndimasinkhasinkha za inu.+ Yesaya 26:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Usiku, mtima wanga umakulakalakani.+ Ndithu ndimakufunafunani ndi mtima wonse,+ chifukwa mukadzaweruza dziko lapansi,+ anthu okhala panthaka ya dzikolo adzaphunzira chilungamo.+
8 Masana Yehova adzalamula kukoma mtima kwake kosatha kuti kufike pa ine,+Ndipo usiku ndidzaimba za iye.+Ndidzapemphera kwa Mulungu wondipatsa moyo.+
9 Usiku, mtima wanga umakulakalakani.+ Ndithu ndimakufunafunani ndi mtima wonse,+ chifukwa mukadzaweruza dziko lapansi,+ anthu okhala panthaka ya dzikolo adzaphunzira chilungamo.+