Yobu 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma palibe wanena kuti, ‘Kodi Mulungu, Wondipanga Wamkulu,+ ali kuti,Amene amapatsa anthu nyimbo usiku?’+ Salimo 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinu malo anga obisalamo, mudzanditeteza ku masautso.+Mudzachititsa kuti chisangalalo chindizungulire pamene mukundipulumutsa.+ [Seʹlah.] Salimo 63:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndikakumbukira inu ndili pabedi langa,+Pa nthawi za ulonda wa usiku* ndimasinkhasinkha za inu.+
10 Koma palibe wanena kuti, ‘Kodi Mulungu, Wondipanga Wamkulu,+ ali kuti,Amene amapatsa anthu nyimbo usiku?’+
7 Ndinu malo anga obisalamo, mudzanditeteza ku masautso.+Mudzachititsa kuti chisangalalo chindizungulire pamene mukundipulumutsa.+ [Seʹlah.]