Salimo 42:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Masana Yehova adzalamula kukoma mtima kwake kosatha kuti kufike pa ine,+Ndipo usiku ndidzaimba za iye.+Ndidzapemphera kwa Mulungu wondipatsa moyo.+ Salimo 77:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Usiku ndidzakumbukira nyimbo zanga zoimbidwa ndi chipangizo cha zingwe.+Ndidzasonyeza kudera nkhawa mumtima mwanga,+Ndipo ndidzasinkhasinkha zinthu zonse mozama. Salimo 149:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu okhulupirika akondwere mu ulemerero.Iwo aimbe mosangalala pamabedi awo.+ Machitidwe 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma chapakati pa usiku,+ Paulo ndi Sila anali kupemphera ndi kutamanda Mulungu poimba nyimbo,+ ndipo akaidi ena anali kuwamva.
8 Masana Yehova adzalamula kukoma mtima kwake kosatha kuti kufike pa ine,+Ndipo usiku ndidzaimba za iye.+Ndidzapemphera kwa Mulungu wondipatsa moyo.+
6 Usiku ndidzakumbukira nyimbo zanga zoimbidwa ndi chipangizo cha zingwe.+Ndidzasonyeza kudera nkhawa mumtima mwanga,+Ndipo ndidzasinkhasinkha zinthu zonse mozama.
25 Koma chapakati pa usiku,+ Paulo ndi Sila anali kupemphera ndi kutamanda Mulungu poimba nyimbo,+ ndipo akaidi ena anali kuwamva.