Salimo 63:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndikakumbukira inu ndili pabedi langa,+Pa nthawi za ulonda wa usiku* ndimasinkhasinkha za inu.+ Salimo 119:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Pakati pa usiku ndimadzuka kuti ndikuyamikeni+Chifukwa cha zigamulo zanu zolungama.+ Luka 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 M’masiku amenewa, Yesu anapita kuphiri kukapemphera,+ ndipo anachezera kupemphera kwa Mulungu usiku wonse.+
12 M’masiku amenewa, Yesu anapita kuphiri kukapemphera,+ ndipo anachezera kupemphera kwa Mulungu usiku wonse.+