Salimo 42:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Masana Yehova adzalamula kukoma mtima kwake kosatha kuti kufike pa ine,+Ndipo usiku ndidzaimba za iye.+Ndidzapemphera kwa Mulungu wondipatsa moyo.+ Machitidwe 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma chapakati pa usiku,+ Paulo ndi Sila anali kupemphera ndi kutamanda Mulungu poimba nyimbo,+ ndipo akaidi ena anali kuwamva.
8 Masana Yehova adzalamula kukoma mtima kwake kosatha kuti kufike pa ine,+Ndipo usiku ndidzaimba za iye.+Ndidzapemphera kwa Mulungu wondipatsa moyo.+
25 Koma chapakati pa usiku,+ Paulo ndi Sila anali kupemphera ndi kutamanda Mulungu poimba nyimbo,+ ndipo akaidi ena anali kuwamva.