Mateyu 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma iwe popemphera, lowa m’chipinda chako pawekha+ ndi kutseka chitseko, ndipo pemphera kwa Atate wako amene ali kosaoneka.+ Ukatero Atate wako amene amaona kuchokera kosaonekako adzakubwezera. Maliko 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako anakwera m’phiri ndi kuitana amene anali kuwafuna,+ ndipo iwo anapita kwa iye.+
6 Koma iwe popemphera, lowa m’chipinda chako pawekha+ ndi kutseka chitseko, ndipo pemphera kwa Atate wako amene ali kosaoneka.+ Ukatero Atate wako amene amaona kuchokera kosaonekako adzakubwezera.