2 Mafumu 4:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndiyeno Elisa analowa m’chipindamo n’kutseka chitseko. M’chipindamo analimo awiriwiri.+ Atatero anayamba kupemphera kwa Yehova.+ Yesaya 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Inu anthu anga, pitani mukalowe m’zipinda zanu zamkati ndipo mukatseke zitseko.+ Mukabisale kwa kanthawi mpaka mkwiyo utadutsa.+
33 Ndiyeno Elisa analowa m’chipindamo n’kutseka chitseko. M’chipindamo analimo awiriwiri.+ Atatero anayamba kupemphera kwa Yehova.+
20 “Inu anthu anga, pitani mukalowe m’zipinda zanu zamkati ndipo mukatseke zitseko.+ Mukabisale kwa kanthawi mpaka mkwiyo utadutsa.+