Salimo 27:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti pa tsiku la tsoka, iye adzandibisa m’malo ake otetezeka.+Adzandibisa m’malo obisika m’hema wake.+Adzandiika pamwamba, pathanthwe.+ Salimo 57:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Ndikomereni mtima inu Mulungu, ndikomereni mtima,+Pakuti ine ndathawira kwa inu.+Ndipo ndathawira mumthunzi wa mapiko anu kufikira masoka atadutsa.+ Salimo 91:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzakutchinjiriza ndi mapiko ake,+Udzathawira pansi pa mapiko ake.+Choonadi chake+ chidzakhala chishango chako+ chachikulu ndi malo ako achitetezo.
5 Pakuti pa tsiku la tsoka, iye adzandibisa m’malo ake otetezeka.+Adzandibisa m’malo obisika m’hema wake.+Adzandiika pamwamba, pathanthwe.+
57 Ndikomereni mtima inu Mulungu, ndikomereni mtima,+Pakuti ine ndathawira kwa inu.+Ndipo ndathawira mumthunzi wa mapiko anu kufikira masoka atadutsa.+
4 Adzakutchinjiriza ndi mapiko ake,+Udzathawira pansi pa mapiko ake.+Choonadi chake+ chidzakhala chishango chako+ chachikulu ndi malo ako achitetezo.