Rute 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova akudalitse chifukwa cha zimene wachita,+ ndipo Yehova, Mulungu wa Isiraeli akufupe mokwanira.+ Iye amene m’mapiko mwake wathawiramo ndi kupezamo chitetezo.”+ Salimo 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndisungeni monga mwana wa diso,+Ndibiseni mumthunzi wa mapiko anu,+ Salimo 63:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti mwandithandiza,+Ndipo mumthunzi wa mapiko anu ndimafuula mosangalala.+
12 Yehova akudalitse chifukwa cha zimene wachita,+ ndipo Yehova, Mulungu wa Isiraeli akufupe mokwanira.+ Iye amene m’mapiko mwake wathawiramo ndi kupezamo chitetezo.”+
8 Ndisungeni monga mwana wa diso,+Ndibiseni mumthunzi wa mapiko anu,+ Salimo 63:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti mwandithandiza,+Ndipo mumthunzi wa mapiko anu ndimafuula mosangalala.+