Deuteronomo 32:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anam’peza m’dziko lachipululu,+M’chipululu chopanda kanthu, molira zilombo zakutchire.+Pamenepo anayamba kum’zungulira,+ kum’samalira,+Kum’teteza monga mwana wa diso lake.+ Zekariya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pambuyo popatsidwa ulemerero,+ Mulungu wandituma kwa anthu a mitundu ina amene anali kukulandani zinthu zanu,+ pakuti Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Amene akukukhudzani,+ akukhudza mwana wa diso langa.+
10 Anam’peza m’dziko lachipululu,+M’chipululu chopanda kanthu, molira zilombo zakutchire.+Pamenepo anayamba kum’zungulira,+ kum’samalira,+Kum’teteza monga mwana wa diso lake.+
8 Pambuyo popatsidwa ulemerero,+ Mulungu wandituma kwa anthu a mitundu ina amene anali kukulandani zinthu zanu,+ pakuti Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Amene akukukhudzani,+ akukhudza mwana wa diso langa.+