Nehemiya 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munawapatsa mzimu wanu wabwino+ kuti akhale anzeru. Simunawamane mana+ ndipo munawapatsa madzi kuti athetse ludzu lawo.+ Salimo 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndimaganiza kuti: Munthu+ ndani kuti muzimuganizira,+Ndipo mwana wa munthu wochokera kufumbi ndani kuti muzimusamalira?+
20 Munawapatsa mzimu wanu wabwino+ kuti akhale anzeru. Simunawamane mana+ ndipo munawapatsa madzi kuti athetse ludzu lawo.+
4 Ndimaganiza kuti: Munthu+ ndani kuti muzimuganizira,+Ndipo mwana wa munthu wochokera kufumbi ndani kuti muzimusamalira?+