Yesaya 51:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ineyo ndi amene ndikukutonthozani anthu inu.+ “Kodi n’chifukwa chiyani iwe ukuopa munthu woti adzafa,+ ndi mwana wa munthu yemwe adzakhale ngati udzu wobiriwira?+ 1 Akorinto 15:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Munthu woyambayo anachokera padziko lapansi ndipo anapangidwa ndi fumbi.+ Wachiwiriyo anachokera kumwamba.+
12 “Ineyo ndi amene ndikukutonthozani anthu inu.+ “Kodi n’chifukwa chiyani iwe ukuopa munthu woti adzafa,+ ndi mwana wa munthu yemwe adzakhale ngati udzu wobiriwira?+
47 Munthu woyambayo anachokera padziko lapansi ndipo anapangidwa ndi fumbi.+ Wachiwiriyo anachokera kumwamba.+