Salimo 90:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwawawonongeratu,+ ndipo amangozimiririka ngati maloto.+M’mawa amakhala ngati msipu wobiriwira umene watsitsimuka.+ Salimo 103:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Masiku a moyo wa munthu ali ngati masiku a udzu wobiriwira.+Iye amaphuka ngati mmene duwa lakutchire limaphukira.+ Yesaya 40:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tamvera! Winawake akunena kuti: “Lankhula mofuula!”+ Ndiye wina akuti: “Ndilankhule mofuula za chiyani?” “Anthu onse ali ngati udzu wobiriwira ndipo kukoma mtima kwawo konse kosatha kuli ngati maluwa akutchire.+ 1 Petulo 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti “anthu onse ali ngati udzu, ndipo ulemerero wawo wonse uli ngati duwa la udzu.+ Udzuwo umafota ndipo duwalo limathothoka,+
5 Mwawawonongeratu,+ ndipo amangozimiririka ngati maloto.+M’mawa amakhala ngati msipu wobiriwira umene watsitsimuka.+
15 Masiku a moyo wa munthu ali ngati masiku a udzu wobiriwira.+Iye amaphuka ngati mmene duwa lakutchire limaphukira.+
6 Tamvera! Winawake akunena kuti: “Lankhula mofuula!”+ Ndiye wina akuti: “Ndilankhule mofuula za chiyani?” “Anthu onse ali ngati udzu wobiriwira ndipo kukoma mtima kwawo konse kosatha kuli ngati maluwa akutchire.+
24 Pakuti “anthu onse ali ngati udzu, ndipo ulemerero wawo wonse uli ngati duwa la udzu.+ Udzuwo umafota ndipo duwalo limathothoka,+