Yobu 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Komanso masiku anga akufulumira kwambiri kuposa munthu wothamanga.+Iwo athawa ndipo ndithu sadzaona zabwino. Yobu 27:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mphepo ya kum’mawa idzamunyamula n’kumusowetsa,+Ndipo idzamuchotsa pamalo pake.+
25 Komanso masiku anga akufulumira kwambiri kuposa munthu wothamanga.+Iwo athawa ndipo ndithu sadzaona zabwino.