Salimo 90:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwawawonongeratu,+ ndipo amangozimiririka ngati maloto.+M’mawa amakhala ngati msipu wobiriwira umene watsitsimuka.+ Yesaya 51:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ineyo ndi amene ndikukutonthozani anthu inu.+ “Kodi n’chifukwa chiyani iwe ukuopa munthu woti adzafa,+ ndi mwana wa munthu yemwe adzakhale ngati udzu wobiriwira?+ 1 Petulo 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti “anthu onse ali ngati udzu, ndipo ulemerero wawo wonse uli ngati duwa la udzu.+ Udzuwo umafota ndipo duwalo limathothoka,+
5 Mwawawonongeratu,+ ndipo amangozimiririka ngati maloto.+M’mawa amakhala ngati msipu wobiriwira umene watsitsimuka.+
12 “Ineyo ndi amene ndikukutonthozani anthu inu.+ “Kodi n’chifukwa chiyani iwe ukuopa munthu woti adzafa,+ ndi mwana wa munthu yemwe adzakhale ngati udzu wobiriwira?+
24 Pakuti “anthu onse ali ngati udzu, ndipo ulemerero wawo wonse uli ngati duwa la udzu.+ Udzuwo umafota ndipo duwalo limathothoka,+