Salimo 118:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova ali kumbali yanga, sindidzaopa.+Munthu wochokera kufumbi angandichite chiyani?+ Miyambo 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kuopa anthu n’kumene kumatchera msampha,+ koma wokhulupirira Yehova adzatetezedwa.+ Danieli 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamenepo Sadirake, Mesake ndi Abedinego anayankha mfumuyo kuti: “Inu mfumu Nebukadinezara, palibenso chimene ife tinganene kwa inu pa nkhani imeneyi.+ Mateyu 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+
16 Pamenepo Sadirake, Mesake ndi Abedinego anayankha mfumuyo kuti: “Inu mfumu Nebukadinezara, palibenso chimene ife tinganene kwa inu pa nkhani imeneyi.+
28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+