Luka 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Akapita nanu kumabwalo amilandu, ndi kwa akuluakulu aboma, komanso kwa olamulira, musade nkhawa kuti mukadziteteza bwanji kapena mukanena chiyani.+ Luka 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chotero tsimikizirani m’mitima yanu kuti musachite kukonzekera zoti mukayankhe podziteteza,+ Machitidwe 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Poyankha Petulo ndi atumwi enawo ananena kuti: “Ife tiyenera kumvera Mulungu monga wolamulira, osati anthu.+
11 Akapita nanu kumabwalo amilandu, ndi kwa akuluakulu aboma, komanso kwa olamulira, musade nkhawa kuti mukadziteteza bwanji kapena mukanena chiyani.+
29 Poyankha Petulo ndi atumwi enawo ananena kuti: “Ife tiyenera kumvera Mulungu monga wolamulira, osati anthu.+