-
Machitidwe 4:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Koma poyankha, Petulo ndi Yohane anawauza kuti: “Weruzani nokha, ngati n’koyenera pamaso pa Mulungu kumvera inu koposa Mulungu.
-