Yohane 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndikukupatsani lamulo latsopano, kuti muzikondana. Mmene ine ndakukonderani,+ inunso muzikondana.+ Yohane 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mukasunga malamulo anga,+ mudzakhalabe m’chikondi changa, monga mmene ine ndasungira malamulo a Atate+ ndi kukhalabe m’chikondi chake. Yakobo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komabe muzichita zimene mawu amanena,+ osati kungomva chabe, n’kumadzinyenga ndi maganizo onama.+ 1 Yohane 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+
34 Ndikukupatsani lamulo latsopano, kuti muzikondana. Mmene ine ndakukonderani,+ inunso muzikondana.+
10 Mukasunga malamulo anga,+ mudzakhalabe m’chikondi changa, monga mmene ine ndasungira malamulo a Atate+ ndi kukhalabe m’chikondi chake.
3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+