Miyambo 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kuchita zinthu zoyenera ndi zachilungamo kumamusangalatsa kwambiri Yehova, kuposa kupereka nsembe.+ Hoseya 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti ndimakondwera ndi kukoma mtima kosatha,+ osati ndi nsembe.+ Ndimakondweranso ndi kudziwa Mulungu, osati ndi nsembe zopsereza zathunthu.+ Maliko 12:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kunena za kukonda Mulungu ndi mtima wonse, maganizo onse, mphamvu zonse, komanso kukonda mnzako mmene umadzikondera wekha, n’zofunika kwambiri kuposa nsembe zonse zopsereza zathunthu ndi nsembe zina.”+
3 Kuchita zinthu zoyenera ndi zachilungamo kumamusangalatsa kwambiri Yehova, kuposa kupereka nsembe.+
6 Pakuti ndimakondwera ndi kukoma mtima kosatha,+ osati ndi nsembe.+ Ndimakondweranso ndi kudziwa Mulungu, osati ndi nsembe zopsereza zathunthu.+
33 Kunena za kukonda Mulungu ndi mtima wonse, maganizo onse, mphamvu zonse, komanso kukonda mnzako mmene umadzikondera wekha, n’zofunika kwambiri kuposa nsembe zonse zopsereza zathunthu ndi nsembe zina.”+