Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 15:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Poyankha Samueli anati: “Kodi Yehova amakondwera ndi nsembe zopsereza+ ndi nsembe zina kuposa kumvera mawu a Yehova? Taona! Kumvera+ kuposa nsembe,+ ndipo kumvetsera mosamala kuposa mafuta+ a nkhosa zamphongo.

  • Salimo 50:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pereka nsembe zoyamikira kwa Mulungu,+

      Ndipo pereka kwa Wam’mwambamwamba zimene walonjeza.+

  • Hoseya 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti ndimakondwera ndi kukoma mtima kosatha,+ osati ndi nsembe.+ Ndimakondweranso ndi kudziwa Mulungu, osati ndi nsembe zopsereza zathunthu.+

  • Mika 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kodi Yehova adzakondwera ndi masauzande a nkhosa zamphongo? Kodi adzakondwera ndi mitsinje ya mafuta masauzande makumimakumi?+ Kapena kodi ndipereke mwana wanga wamwamuna woyamba kubadwa chifukwa cha cholakwa changa?+ Kodi ndipereke chipatso cha mimba yanga chifukwa cha tchimo langa?

  • Mateyu 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Komabe, ngati mukanamvetsa tanthauzo la mawu akuti, ‘Ndikufuna chifundo,+ osati nsembe,’+ simukanaweruza anthu osalakwa.

  • Maliko 12:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Kunena za kukonda Mulungu ndi mtima wonse, maganizo onse, mphamvu zonse, komanso kukonda mnzako mmene umadzikondera wekha, n’zofunika kwambiri kuposa nsembe zonse zopsereza zathunthu ndi nsembe zina.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena